• 1
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0

2010 - LP
#

Intro
I represent/ my family/ 25 / n Malawi
Verse 1
Choyambilira ndimakonda my family
Azinzanga we all live happily
In the studio ndimomwe ndimafila boo/ alotta haters
But there is no stopping me
Ndimachokera ku ghetto u feelin me/ 25B
Bwoi better fear me
Better yet/ don’t interfere B
Ndili busy my life is not easy
Sometimes it gets a little crazy
Sindiyiwala Mulungu ine ndimaphreza
Namalenga Leza Jehovah
Phyzo Phyzix am telling you its ova
Bridge
I represent my people every day/ ay
They got ma back when trouble come my way/ ay
It don’t matter what them haters say/ ay
I won’t stop
Hook
I Represent
Ndi zomwe ndimapanga
For ma people
Ndi zomwe ndimapanga
I work hard
Ndi zomwe ndimapanga
Kulimbikira ntchito ndi zomwe ndimapanga x2
Verse 2
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni
Mani Phyzo ndi man on a mission
It was a vision to be on Television
Nchifukwa chake ndimamveka Malawian
Ma alien mukumaflowa American
Ama do what I can am an African
Ndikuonetsani kuti ndine Man-Man
Main Man ndimakonda ma women
Kuwakonda sindekuti kuwafunsira
Ndimayamika mabebi ndi maluwa
Makamaka opanga zolawula
Hook
I Represent
Ndi zomwe ndimapanga
For ma people
Ndi zomwe ndimapanga
I work hard
Ndi zomwe ndimapanga
Kulimbikira ntchito ndi zomwe ndimapanga x2
Verse 3
Ndine George wa mu Jungle
Osati Bush
Ndakula ndi mwambo ndinapita ku Jando
Ine ndi Phyzo Rambo wa nyimbo
Ukandifuna undisearcher pa Google
Ndine wotchuka ngati game ya football
Bluetooth yanga siimafuna dongle
Ndimamenya connect ndimamemba
Odya bwino ndi mamemba a matemba
The Real elements gave me the baton
After Nyambo cholapitsa was put on
Am a ghetto MC whose relevant
You can call me the 5th Real Element
Bridge
I represent my people every day/ ay
They got ma back when trouble come my way/ ay
It don’t matter what them haters say/ ay
I won’t stop
Hook
I Represent
Ndi zomwe ndimapanga
For ma people
Ndi zomwe ndimapanga
I work hard
Ndi zomwe ndimapanga
Kulimbikira ntchito ndi zomwe ndimapanga x2

Recently Listened by

0 comments
    No comments found

:: / ::
::
/ ::

Queue