• 4
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0

2010 - LP
#

Intro
Mani Phyzo/ Town Monger
Prelude
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni
Verse 1
Ine sindidya nsima/ Ine koma Rice
Kudya kwa mtauni ndi Chicken and Chips
Ukafuna kuthima Malawi Gin Juice
Nthawi zina moyo umakhala very nicey
Kuchita kukoma ngati wathira ka spicey
Makamaka ukagwira tchiki/ ka wifey
Koti kamafewa komathanso massage
Kuti kadzindipanga ndikachoka pa stage
Bukhu ndi lomwe lija/ different page
Ndidali wa chibwana/ pano mature age
Ndachepetsa rage/ ndikuimba za kheshi
Feeling very lucky Bwera tipange betchi
Interlude
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni
Hook
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
City Boy Rasta
Ndine mfana wa Doroba
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
Malawian Gangsta
Ndine mfana wa Doroba
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
City Boy Rasta
Ndine mfana wa Doroba
Bridge
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni
Verse 2
Mabebi/ a doroba ndi ma armed robber
Amaba/ moopseza ndi zida zobisika/ zochitika
Short time nde ikugulika
Kupita kubala ngati kuti uli ku msika
Mabebi/ kuzigulitsa ngati kaunjika
Mamemba/ nkumagula ngati ndi kaunjika
Fanzi yokonda Kudya/ siimakonda kuphika
Amakonda kupakula chabe nsima ikatchakuka
Amabwera pa cooker kapena pa mafuwa
Ukapanga achieve_amadzangomwa thukuta
Chonchonso/ moyo uli ndi mafana otchera
Amayamba kubwera/ ukayamba kudyelera
Interlude
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni
Hook
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
City Boy Rasta
Ndine mfana wa Doroba
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
Malawian Gangsta
Ndine mfana wa Doroba
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
City Boy Rasta
Ndine mfana wa Doroba
Bridge
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni
Verse 3
Ena mwa ife tilibe passipoti
Tilibe manyumba/ Tilibe mapuloti
Nyumba yomwe timakhala ndi ya landilodi
Odi/ akubwera kudzatenga rent
Muthawira kuti kodi mupita kuti
Poti ndinu a mtauni mulibe kumudzi
Interlude
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni
Hook
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
City Boy Rasta
Ndine mfana wa Doroba
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
Malawian Gangsta
Ndine mfana wa Doroba
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
City Boy Rasta
Ndine mfana wa Doroba
Bridge
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
City Boy Rasta
Ndine mfana wa Doroba
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
Malawian Gangsta
Ndine mfana wa Doroba
Ndine Town Monger
Ndine Town Monger
City Boy Rasta
Ndine mfana wa Doroba
Bridge
Sindidafune kukhala wa chitauni
Kungoti ndidakulira mtauni

Recently Listened by

0 comments
    No comments found

:: / ::
::
/ ::

Queue