Verse 1
Ndikambeko nkhani ya muno mtauni
Tcherani/ makutu/ ndikuuzeni
Momwe timakhalira zimatichitikira
Palibe kudyelera
Osalimbikira
Ukakhala wokongola zimakuyendera
Pali fanzi iwiri yomwe imaiifira/ life
Wolemera ndi wokongola
Zimafunika kukhala wa dollar
Mfana wa maluzi amati ndi wa mbola
Bola/ chola/ ukamachitola
Sizimavuta kulipira/ lobola
Olo kugula ka njale ka Corolla
Bridge
I gotta be rich to survive out here
I gotta be beautiful to be out here
I gotta be rich to survive out here
I gotta be beautiful to be out here
Interlude
I gotta be rich or fall in a ditch
I gotta be rich or fall in a ditch
Hook
Moyo ndi Wokondera
Moyo ndi Wokondera
I gotta be rich to survive out here
I gotta be beautiful to be out here
Moyo ndi Wokondera
Moyo ndi Wokondera
I gotta be rich to survive out here
I gotta be beautiful to be out here
Verse 2
Moyo wa doroba umafuna hustle
Ukhale/ ngati Mkango uli mu Jungle
Kapena/ ngati Rambo ali pa Nkhondo
Kumakhala Shasha osanong’oneza bondo
Kukhala munthu wa mfundo sizinthu za wamba
Ineyo/ ndine Phyzo ndipo ndine woyimba
Iweyo/ ndiwe nda ndipo umapanga cha?
Tanena/ ndiwe original kapena wo burner?
Pa mirror ndipomwe ndimaona ndine wowilira
Moyowu/ umafunika kukhala wopilira
Akati; ‘Shasha ndi nda?’
Ine ndimayimilira!
Akati; ‘Nyatwa ndi nda?’
Ine ndimayimilira!
Bridge
I gotta be rich to survive out here
I gotta be beautiful to be out here
I gotta be rich to survive out here
I gotta be beautiful to be out here
Interlude
I gotta be rich or fall in a ditch
I gotta be rich or fall in a ditch
Hook
Moyo ndi Wokondera
Moyo ndi Wokondera
I gotta be rich to survive out here
I gotta be beautiful to be out here
Moyo ndi Wokondera
Moyo ndi Wokondera
I gotta be rich to survive out here
I gotta be beautiful to be out here