• 5
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0

2010 - LP
#

Verse 1
Mkazi
Amafuna kiss osati kitsi
Osamububuda milomo tangomukisse
Haggi
Isakhale ngati wagwira jaggi
Palibe defence m’phwanga panga attacki
Posi
Osakhala ngati teapot
Mukafika pamalo perekani reporti
Hotti
Ifeyo ndi afana a hotti
Aliyense wavomereza ngati voti
Poti
Ena mwa inu ndi ma Robotti
Ma DVD player opanda remote
Odi
Tsekula before am goni
Ineyo ndi chance ndimabwera kamodzi
Nsanje
Ili khathi khathi ngati mkaka
Imandipatsa Energy ngati ndi makaka
Trust me Kaka ndili ngati Mulaka
I’ll make hits mpakana mpaka
Hook
Ma Problem / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Girlfriend / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Boyfriend/ Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Landlord / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
Verse 2
Chaka chake ndichino tikolora
Tidzala ndalama ndipo zimera
Tigwira mabebi osati mbwera
Tiziweleweta no more mbwelera
Akafuna mfundo tizizikamba
Tchiki ya boo ndi tantanana
D’banji amati sweeti Banana
Ndimaswa bakera osati mbama
Yes I can ngati Obama
I don’t bring comedy I bring Drama
This here music is melodrama
Panopa ndi nthawi yozisaka/….
Ndi quarter pasti kuzisaka
Kumapanga changu champhaka
When am in Jozi I’ll be a Tsotsi
Dollar ya pamwezi ndi ulesi
Hook
Ma Problem / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Girlfriend / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Boyfriend/ Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Landlord / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
Verse 3
Madzi asiya pa chitsime
Magetsi athima tikathime
Galimoto ayi tibabade
Tiyende wapansi wa mabade
Ndege zikadula tiuluke
Tipeze chifukwa chotambila
Phone ikati call later
Ifeyo tijothe makalata
Osadziphoda iweyo si mkazi
Vomereza m’phwanga ndiwe wakuda basi
Osatinyenga kuti uli ngati Ghandi
Just accept that your ass is broke
Pakakhala ntchito/ we apply
Ikakhala demandi/ we supply
Pakakhala vuto/ we reply
Akatigwira nazo/ we deny
Hook
Ma Problem / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Girlfriend / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Boyfriend/ Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata
My Landlord / Satapata
Panopa ndi/ Hakuna Matata

Recently Listened by

0 comments
    No comments found

:: / ::
::
/ ::

Queue