• 2
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0

2010 - LP
#

Intro
Kape ndi Kape
Kape/ Kape ndi Kape eh x4
Verse 1
Zomangotchila pakati pa matchiki/ ndi ukape
Zomangokhala pakati pa magaye/ ndi ukape
Kumakula bwa?
Tapita pita ukazisake
Kumangokhala pa deni pa masteni/ ndi ukape
Kumathamanga thamanga
Kumazisaka saka
Osamangophwanyilira/ osamangophakilira
Osamangomva sugar
Osamangokombezera
Zikokoto za mpunga daily m’mamawa kukacha
Osamangokhala opusa
Mani mudzichenjera
Osamangotokota/ zidzakumenyetsani
Osamangopemphapempha/ zidzakunyozetsani
Osamangofunda funda kumamva kutenthera
Akudzalanda eni ake bulanyanyalo
Akakuputa kape/ osamusekelera
Akakunyoza makape/ osawasekelera
Adzayesa kuti mwina ndiwe size yawo
Hook
Olo atchene
Olo asambe
Olo agwire
Olo atchuke
Kape ndi Kape
Kape/ Kape ndi Kape eh x2
Olo atchene
Olo asambe
Olo agwire
Olo atchuke
Kape ndi Kape
Kape/ Kape ndi Kape eh x2
Verse 2
Kape ndi Kape/ olo atchene olo asatchene
Kape ndi Kape olo atchuke olo asatchuke
Akumatotaa?/ akumatotokota
Akumatodzipopa kuti iwowo nde amboba/ eh
Mani Phyzonso siziwakhudza amangotchila aise
Kundinyoza aise/ sindimayankha aise/ aise
Kumandinena kumbali ndi za ukape basi
Kuma damager kwa tchiki/ ndi za ukape basi
Osamabwera pa bawa/ ngati ulibe ndalama
Mani Phyzo has a farm/ ire iree ireee oh
Ndimadzalapo mbeu za ma ire a boo
Chaka chino tionetsana ine ndi zobanduka
Hook
Olo atchene
Olo asambe
Olo agwire
Olo atchuke
Kape ndi Kape
Kape/ Kape ndi Kape eh x2
Olo atchene
Olo asambe
Olo agwire
Olo atchuke
Kape ndi Kape
Kape/ Kape ndi Kape eh x2
Bridge
Za ukape basi
Za zaukape basi x4
Verse 3
Shasha ndi shasha
Dolo ndi dolo
Nyatwa ndi Nyatwa
Nyenti ndi nyenti
Kape ndi Kape
Kape/ Kape ndi Kape eh x2
Ukafuna revenge
Kumangolimbikira
Zimawawa makape/ ukamachita boo
Kumapemphera koma/ adzakuzimitsa
Adzakuchita load-shedding ya Escom
Hook
Olo atchene
Olo asambe
Olo agwire
Olo atchuke
Kape ndi Kape
Kape/ Kape ndi Kape eh x2
Olo atchene
Olo asambe
Olo agwire
Olo atchuke
Kape ndi Kape
Kape/ Kape ndi Kape eh x2

Recently Listened by

0 comments
    No comments found

:: / ::
::
/ ::

Queue