Intro
Nthumwi Piksy Tapps
Zikafika Zolapitsa The celebration
Tenga nkhope yako bisa of a Malawian Hip Hop
Ona zikuthamangitsa Classic
Umyata mfana umyata let’s go yo!
Phyzix: Mfumu ya zi Nyau Tay Grin: Tay Grin!
Phyzix: Mfumu ya ma Gamba Phyzix: Mani Phyzo!
Phyzix: Mfumu ya ma Dolo Young Kay: Young Kay!
Phyzix: Mafumu a Sendeza Atumwi: Atumwi!
Verse 1 (Phyzix)
Chenicheni chabweranso kachikena
Umyata mfana unagena
Ndinamera mapiko ndimaflyer
Pakati pa iwe ndi ine I am more flyer
Kutchuka kumakongoletsa
Memba yonyasa akuichaser
Ndiponso ndikudabadira
Mani Phyzo mphwanga ngo limbikira
Manzi sindidzaisiya/ pa Malawi pano ndine Pioneer
Mamemba akandishosha
Sindimawaimba ndimawaphika
Zopusa sindimaimba
Ine ndi wolusa ndine wa mu gutta
Ineyo ndine ma Phyzo
Chomwe ndimatha ndi makata
Hook (Nthumwi Piksy)
Ndangochoka pongomaliza kafukufuku
Eh mafana mukuchulutsa matukutuku
Kunena kwanu mukuchepetsa mithutha
Thawa pamalo Nkhondo yavuta
Zikafika Zolapitsa/ Umyata
Tenga nkhope yako bisa/ Umyata
Ona zikuthamangitsa/ Umyata
Umyata mfana Umyata
Verse 2 (Tay Grin)
Am the maestro of this rap game
Dressed to kill MCs am murdering
Paid enough attention now its dividends
Gamba wa ku Dowa/ Shasha pa ku flowa/ flowa
Like Johnny Walker/ I walk the talk
Boss over here with a tailored-flow
High grade export/ Swagger marinated
Execution on point like I seem stressed
I do it for the love but more for the business
Study my moves so maybe you can get in this
Y’ all gossip like chicks am staying clear
My hustle is for the cash am going hard
Real recognize real that’s why we here recording
Hustle constant like a full-court press
I put pressure on the game fake MCs on a bench
MVP over here/ Yes!
Hook (Nthumwi Piksy)
Ndangochoka pongomaliza kafukufuku
Eh mafana mukuchulutsa matukutuku
Kunena kwanu mukuchepetsa mithutha
Thawa pamalo Nkhondo yavuta
Zikafika Zolapitsa/ Umyata
Tenga nkhope yako bisa/ Umyata
Ona zikuthamangitsa/ Umyata
Umyata mfana Umyata
Verse 3 (Young Kay)
Izi mani ndi zenizeni
Ku nkhani yoyimba envied by many men
Every verse thunder n lightning/ hurricane
If you need help making a hit/ ndiimbileni
I hold the top five spots on your top ten
Best believe I leave any word I’ve spoken
The Mic is a fire what I spit is propane
I also got it from my poppa like Progain
Oh man/ ndine shasha
Anthu atopa ndi ti nyimbo tosasa
Flyer than Eagle/ Eagle waguan Rasta
Whatever test I ace opanda likasa
I am the answer
As far as strikes there are none
Trust me a bad man akupanga makani ndani?
My words are daggers cutting a beat’s life span
Ahead of y’all so I slow it down whenever I can
Hook (Nthumwi Piksy)
Ndangochoka pongomaliza kafukufuku
Eh mafana mukuchulutsa matukutuku
Kunena kwanu mukuchepetsa mithutha
Thawa pamalo Nkhondo yavuta
Zikafika Zolapitsa/ Umyata
Tenga nkhope yako bisa/ Umyata
Ona zikuthamangitsa/ Umyata
Umyata mfana Umyata
Outro
Cholapitsa remix/ Zolapitsa
Young Kay, Tay Grin, Atumwi and me/ Mani Phyzo/ Mr Phyzix
Good looking out Dare Devilz; Marcus and GD for the Beat man
It’s Tapps on the boards/ The Mayor/ U & me man let’s run this city
Before my second album comes out; we had to celebrate Cholapitsa
It’s been a hit since 2006/ I mean ha
I still get encores up to now at shows man
Ha ha ha/ ma Phyzo rhythms
You know I started a movement with this song
Panopo fanzi kumangoti mu zi beats
Ine ndine ichi ine chotani chotere/ chotere
All because of Cholapitsa man
Y’all peoples need to recognize ha
From the Ghetto/ ma Phyzo